Yehova Amatithandiza

Yehova Amatithandiza 歌词

原文语言ZU
浏览量36
歌词坐标

原文歌词

ZU
暂时没有翻译,当前显示原文歌词。
18
Ndinkachitadi mantha Ndinali wosatetezeka Ndinkatsutsidwa kwambiri Koma ndalimba mtima Iye wati ndim’dalire Ndithu anditeteza Amandikondadi Wan’thandiza Kulimba n’tafooka Kulimba n’tatha nzeru Kulimba m’mayesero Kupirira ndithu Kulimba m’mavuto Kum’dalira nthawi zonse Yehova ’mandithandiza Wan’dziwitsa Njira zake Zomwe n’zolungama An’thandiza Kuti ndimvetse N’kudziperekabe Sulitu wekha Ngakhale unachoka Ali nawe Akuthandiza Kuti upirirebe ndithu N’kukupatsa nzeru Akuthandiza Kulimba ukafo’ka Kulimba zikavuta Kulimba m’mayesero Kupirira ndithu Kulimba m’mavuto Kum’dalira nthawi zonse Yehova ’matithandiza​ M’zonse, m’zonse Yehova ’matithandiza Tadziwatu ndithu Njira zake Zomwe n’zolungama Yehova ’matithandiza Athandiza Kuti timvetse N’kudziperekabe Ndinatha Kulimba n’tafooka Kulimba n’tatha nzeru Kulimba m’mayesero Kupirira ndithu Kulimba m’mavuto Kum’dalira nthawi zonse Yehova ’matithandiza​ M’zonse, m’zonse Yehova ’matithandiza​ M’zonse, m’zonse Yehova ’matithandiza